Levitiko 26:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Mizinda yanu ndidzaiwononga ndi lupanga+ ndipo malo anu opatulika adzakhala opanda anthu,+ komanso sindidzalandira nsembe zanu zafungo lokhazika mtima pansi.+ Mateyu 24:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma iye anawayankha kuti: “Kodi simukuziona zinthu zonsezi? Ndithu ndikukuuzani, Pano sipadzatsala mwala uliwonse pamwamba pa mwala unzake umene sudzagwetsedwa.”+ Luka 21:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho iye anati: “Kunena za zinthu izi mukuzionazi, masiku adzafika pamene sipadzakhala mwala wosiyidwa pano pamwamba pa mwala unzake umene sudzagwetsedwa.”+
31 Mizinda yanu ndidzaiwononga ndi lupanga+ ndipo malo anu opatulika adzakhala opanda anthu,+ komanso sindidzalandira nsembe zanu zafungo lokhazika mtima pansi.+
2 Koma iye anawayankha kuti: “Kodi simukuziona zinthu zonsezi? Ndithu ndikukuuzani, Pano sipadzatsala mwala uliwonse pamwamba pa mwala unzake umene sudzagwetsedwa.”+
6 Choncho iye anati: “Kunena za zinthu izi mukuzionazi, masiku adzafika pamene sipadzakhala mwala wosiyidwa pano pamwamba pa mwala unzake umene sudzagwetsedwa.”+