Mateyu 26:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mafuta amenewa akanagulitsidwa ndalama zambiri ndipo ndalamazo zikanaperekedwa kwa anthu osauka.”+ Yohane 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “N’chifukwa chiyani mafuta onunkhirawa+ sanagulitsidwe madinari 300 ndi kupereka ndalamazo kwa anthu osauka?”+
5 “N’chifukwa chiyani mafuta onunkhirawa+ sanagulitsidwe madinari 300 ndi kupereka ndalamazo kwa anthu osauka?”+