Maliko 14:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakuti mafuta onunkhirawa akanagulitsidwa ndalama zoposa madinari 300 n’kuzipereka kwa osauka!” Chotero iwo anakhumudwa kwambiri ndi mayiyo.+ Yohane 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “N’chifukwa chiyani mafuta onunkhirawa+ sanagulitsidwe madinari 300 ndi kupereka ndalamazo kwa anthu osauka?”+
5 Pakuti mafuta onunkhirawa akanagulitsidwa ndalama zoposa madinari 300 n’kuzipereka kwa osauka!” Chotero iwo anakhumudwa kwambiri ndi mayiyo.+
5 “N’chifukwa chiyani mafuta onunkhirawa+ sanagulitsidwe madinari 300 ndi kupereka ndalamazo kwa anthu osauka?”+