Mateyu 19:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yesu anamuuza kuti: “Ngati ukufuna kukhala wangwiro, pita kagulitse katundu wako ndipo ndalama zake upatse osauka. Ukatero udzakhala ndi chuma kumwamba,+ ndiyeno ubwere udzakhale wotsatira wanga.”+ Maliko 14:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakuti mafuta onunkhirawa akanagulitsidwa ndalama zoposa madinari 300 n’kuzipereka kwa osauka!” Chotero iwo anakhumudwa kwambiri ndi mayiyo.+
21 Yesu anamuuza kuti: “Ngati ukufuna kukhala wangwiro, pita kagulitse katundu wako ndipo ndalama zake upatse osauka. Ukatero udzakhala ndi chuma kumwamba,+ ndiyeno ubwere udzakhale wotsatira wanga.”+
5 Pakuti mafuta onunkhirawa akanagulitsidwa ndalama zoposa madinari 300 n’kuzipereka kwa osauka!” Chotero iwo anakhumudwa kwambiri ndi mayiyo.+