Mateyu 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Khamu la anthulo litaona zimenezi, linagwidwa ndi mantha ndipo linatamanda Mulungu,+ amene anapereka mphamvu zimenezo+ kwa anthu. Luka 5:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pamenepo anthu onsewo anadabwa kwambiri,+ ndipo anayamba kutamanda Mulungu, mwakuti anagwidwa ndi mantha. Iwo anali kunena kuti: “Taona zodabwitsa lero!”+
8 Khamu la anthulo litaona zimenezi, linagwidwa ndi mantha ndipo linatamanda Mulungu,+ amene anapereka mphamvu zimenezo+ kwa anthu.
26 Pamenepo anthu onsewo anadabwa kwambiri,+ ndipo anayamba kutamanda Mulungu, mwakuti anagwidwa ndi mantha. Iwo anali kunena kuti: “Taona zodabwitsa lero!”+