Mateyu 27:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pilato anafunsanso kuti: “Nanga Yesu, uja amamuti Khristu, ndichite naye chiyani?” Onse anayankha kuti: “Apachikidwe ameneyo!”+ Luka 23:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pilato analankhula nawo kachiwiri, chifukwa anali wofunitsitsa kumasula Yesu.+
22 Pilato anafunsanso kuti: “Nanga Yesu, uja amamuti Khristu, ndichite naye chiyani?” Onse anayankha kuti: “Apachikidwe ameneyo!”+