Luka 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pa tsiku loyamba la mlungu, amayi aja analawirira m’mawa kwambiri kupita kumandako, atatenga zonunkhira zimene anakonza zija.+
24 Pa tsiku loyamba la mlungu, amayi aja analawirira m’mawa kwambiri kupita kumandako, atatenga zonunkhira zimene anakonza zija.+