Mateyu 28:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Tsiku la sabata litatha, m’bandakucha wa tsiku loyamba la mlunguwo, Mariya Mmagadala ndi Mariya wina uja anabwera kudzaona manda.+ Maliko 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho tsiku la sabata+ litapita, Mariya Mmagadala,+ Mariya mayi wa Yakobo, ndi Salome anagula zonunkhira kuti akapake thupi la Yesu.+ Yohane 20:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsiku loyamba+ la mlunguwo, Mariya Mmagadala anabwera kumanda achikumbutsowo m’mawa kwambiri, kudakali mdima, ndipo anaona kuti mwala wachotsedwa kale pamanda achikumbutsowo.+
28 Tsiku la sabata litatha, m’bandakucha wa tsiku loyamba la mlunguwo, Mariya Mmagadala ndi Mariya wina uja anabwera kudzaona manda.+
16 Choncho tsiku la sabata+ litapita, Mariya Mmagadala,+ Mariya mayi wa Yakobo, ndi Salome anagula zonunkhira kuti akapake thupi la Yesu.+
20 Tsiku loyamba+ la mlunguwo, Mariya Mmagadala anabwera kumanda achikumbutsowo m’mawa kwambiri, kudakali mdima, ndipo anaona kuti mwala wachotsedwa kale pamanda achikumbutsowo.+