Maliko 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho tsiku la sabata+ litapita, Mariya Mmagadala,+ Mariya mayi wa Yakobo, ndi Salome anagula zonunkhira kuti akapake thupi la Yesu.+ Luka 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pa tsiku loyamba la mlungu, amayi aja analawirira m’mawa kwambiri kupita kumandako, atatenga zonunkhira zimene anakonza zija.+ Luka 24:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Amayiwa anali Mariya Mmagadala, Jowana+ ndi Mariya mayi wa Yakobo. Komanso amayi+ ena onse amene anali nawo pamodzi anali kuuza atumwi zinthu zimenezi. Yohane 20:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsiku loyamba+ la mlunguwo, Mariya Mmagadala anabwera kumanda achikumbutsowo m’mawa kwambiri, kudakali mdima, ndipo anaona kuti mwala wachotsedwa kale pamanda achikumbutsowo.+
16 Choncho tsiku la sabata+ litapita, Mariya Mmagadala,+ Mariya mayi wa Yakobo, ndi Salome anagula zonunkhira kuti akapake thupi la Yesu.+
24 Pa tsiku loyamba la mlungu, amayi aja analawirira m’mawa kwambiri kupita kumandako, atatenga zonunkhira zimene anakonza zija.+
10 Amayiwa anali Mariya Mmagadala, Jowana+ ndi Mariya mayi wa Yakobo. Komanso amayi+ ena onse amene anali nawo pamodzi anali kuuza atumwi zinthu zimenezi.
20 Tsiku loyamba+ la mlunguwo, Mariya Mmagadala anabwera kumanda achikumbutsowo m’mawa kwambiri, kudakali mdima, ndipo anaona kuti mwala wachotsedwa kale pamanda achikumbutsowo.+