Mateyu 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pakuti Mwana wa munthu+ ndiye Mbuye wa sabata.”+ Luka 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako anapitiriza kuwauza kuti: “Mwana wa munthu ndiye Mbuye wa sabata.”+