Mateyu 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pakuti Mwana wa munthu+ ndiye Mbuye wa sabata.”+ Maliko 2:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Choncho Mwana wa munthu ndiye Mbuye wa sabata.”+