Maliko 9:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ophunzirawo sanali kumvetsa mawuwa, ndipo anali kuopa kumufunsa.+ Yohane 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yesu ananena fanizoli kwa iwo, koma iwo sanadziwe tanthauzo la zinthu zimene anali kuwauzazo.+