Mateyu 22:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pakuti pouka kwa akufa, amuna sadzakwatira ndipo akazi sadzakwatiwa,+ koma adzakhala ngati angelo akumwamba. Maliko 12:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Akadzauka kwa akufa, amuna sadzakwatira ndipo akazi sadzakwatiwa, koma adzakhala ngati angelo akumwamba.+ Yohane 5:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 ndipo adzatuluka. Amene anali kuchita zabwino adzauka kuti alandire moyo.+ Amene anali kuchita zoipa adzauka kuti aweruzidwe.+
30 Pakuti pouka kwa akufa, amuna sadzakwatira ndipo akazi sadzakwatiwa,+ koma adzakhala ngati angelo akumwamba.
25 Akadzauka kwa akufa, amuna sadzakwatira ndipo akazi sadzakwatiwa, koma adzakhala ngati angelo akumwamba.+
29 ndipo adzatuluka. Amene anali kuchita zabwino adzauka kuti alandire moyo.+ Amene anali kuchita zoipa adzauka kuti aweruzidwe.+