Maliko 12:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Davideyo anamutcha kuti ‘Ambuye,’ nanga zikutheka bwanji kuti alinso mwana wake?”+ Ndipo khamu lalikulu linali kumumvetsera mosangalala.+ Luka 19:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Komabe anasowa chochita chifukwa anthu ambiri anali kungomuunjirira kuti amumvetsere ndipo sanali kusiyana naye.+
37 Davideyo anamutcha kuti ‘Ambuye,’ nanga zikutheka bwanji kuti alinso mwana wake?”+ Ndipo khamu lalikulu linali kumumvetsera mosangalala.+
48 Komabe anasowa chochita chifukwa anthu ambiri anali kungomuunjirira kuti amumvetsere ndipo sanali kusiyana naye.+