Luka 13:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Komanso, anthu adzabwera kuchokera kumbali za kum’mawa ndi kumadzulo, kumpoto ndi kum’mwera,+ ndipo adzadya patebulo mu ufumu wa Mulungu.+ Luka 14:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Atamva izi, mmodzi wa alendo anzake anamuuza kuti: “Wodala ndi munthu wakudya chakudya mu ufumu wa Mulungu.”+
29 Komanso, anthu adzabwera kuchokera kumbali za kum’mawa ndi kumadzulo, kumpoto ndi kum’mwera,+ ndipo adzadya patebulo mu ufumu wa Mulungu.+
15 Atamva izi, mmodzi wa alendo anzake anamuuza kuti: “Wodala ndi munthu wakudya chakudya mu ufumu wa Mulungu.”+