Mateyu 20:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma Yesu anawaitana n’kuwauza kuti: “Inu mukudziwa kuti olamulira a anthu a mitundu ina amapondereza anthu awo ndipo akuluakulu amasonyeza mphamvu zawo pa iwo.+ Maliko 10:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Koma Yesu anawaitana, ndipo atafika kwa iye, anawauza kuti: “Inu mukudziwa kuti amene amaoneka ngati akulamulira anthu a mitundu ina amapondereza anthu awo ndipo akuluakulu awo amasonyeza mphamvu zawo pa iwo.+
25 Koma Yesu anawaitana n’kuwauza kuti: “Inu mukudziwa kuti olamulira a anthu a mitundu ina amapondereza anthu awo ndipo akuluakulu amasonyeza mphamvu zawo pa iwo.+
42 Koma Yesu anawaitana, ndipo atafika kwa iye, anawauza kuti: “Inu mukudziwa kuti amene amaoneka ngati akulamulira anthu a mitundu ina amapondereza anthu awo ndipo akuluakulu awo amasonyeza mphamvu zawo pa iwo.+