Mateyu 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Musatenge golide, siliva kapena mkuwa m’zikwama zanu za ndalama.+ Maliko 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Komanso, anawalangiza kuti asanyamule kanthu pa ulendowo kupatulapo ndodo yokha basi. Anawalangiza kuti asatenge mkate, thumba la chakudya,+ kapena ndalama m’zikwama zawo,+ Luka 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye anawauza kuti: “Musanyamule kanthu pa ulendowu, musatenge ndodo, kapena thumba la chakudya, kapena mkate, kapena ndalama zasiliva, kapena kutenga malaya awiri amkati.+
8 Komanso, anawalangiza kuti asanyamule kanthu pa ulendowo kupatulapo ndodo yokha basi. Anawalangiza kuti asatenge mkate, thumba la chakudya,+ kapena ndalama m’zikwama zawo,+
3 Iye anawauza kuti: “Musanyamule kanthu pa ulendowu, musatenge ndodo, kapena thumba la chakudya, kapena mkate, kapena ndalama zasiliva, kapena kutenga malaya awiri amkati.+