Mateyu 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ufumu+ wanu ubwere. Chifuniro chanu+ chichitike, monga kumwamba, chimodzimodzinso pansi pano.+ Maliko 14:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Kenako anati: “Abba,* Atate,+ zinthu zonse n’zotheka kwa inu. Ndichotsereni kapu iyi. Komatu osati mwa kufuna kwanga, koma mwa kufuna kwanu.”+ Yohane 5:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ine sindingachite chilichonse chongoganiza ndekha. Ndimaweruza malinga ndi mmene ndamvera, ndipo chiweruzo chimene ndimapereka n’cholungama,+ chifukwa sinditsatira chifuniro changa, koma chifuniro+ cha amene anandituma. Yohane 6:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Chifukwa ndinatsika kuchokera kumwamba+ kudzachita chifuniro cha iye amene anandituma, osati chifuniro changa.+
36 Kenako anati: “Abba,* Atate,+ zinthu zonse n’zotheka kwa inu. Ndichotsereni kapu iyi. Komatu osati mwa kufuna kwanga, koma mwa kufuna kwanu.”+
30 Ine sindingachite chilichonse chongoganiza ndekha. Ndimaweruza malinga ndi mmene ndamvera, ndipo chiweruzo chimene ndimapereka n’cholungama,+ chifukwa sinditsatira chifuniro changa, koma chifuniro+ cha amene anandituma.
38 Chifukwa ndinatsika kuchokera kumwamba+ kudzachita chifuniro cha iye amene anandituma, osati chifuniro changa.+