Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 26:58
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 58 Koma Petulo anali kumutsatirabe chapatali ndithu, mpaka anafika m’bwalo lamkati+ kunyumba ya mkulu wa ansembeyo. Atalowa mkatimo, anakhala pansi pamodzi ndi antchito a m’nyumbamo kuti aone zotsatira zake.+

  • Maliko 14:54
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 54 Koma Petulo, anali kum’tsatira chapatali ndithu,+ mpaka anafika m’bwalo lamkati kunyumba ya mkulu wa ansembe. Kumeneko iye anakhala pansi pamodzi ndi antchito a m’nyumbamo, n’kumawotha moto walawilawi.

  • Yohane 18:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Tsopano Simoni Petulo ndiponso wophunzira wina anali kutsatira Yesu.+ Wophunzira winayu anali wodziwika kwa mkulu wa ansembe, chotero analowa pamodzi ndi Yesu m’bwalo lamkati kunyumba ya mkulu wa ansembe.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena