Salimo 44:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chifukwa cha mawu a munthu wonditonza ndi wolankhula zachipongwe,Ndiponso chifukwa cha mdani wanga ndi wofuna kundibwezera choipa.+ Yesaya 51:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Ndimvereni, inu odziwa chilungamo, inu amene muli ndi lamulo langa mumtima mwanu.+ Musaope chitonzo cha anthu ndipo musachite mantha chifukwa cha mawu awo onyoza.+
16 Chifukwa cha mawu a munthu wonditonza ndi wolankhula zachipongwe,Ndiponso chifukwa cha mdani wanga ndi wofuna kundibwezera choipa.+
7 “Ndimvereni, inu odziwa chilungamo, inu amene muli ndi lamulo langa mumtima mwanu.+ Musaope chitonzo cha anthu ndipo musachite mantha chifukwa cha mawu awo onyoza.+