Salimo 39:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Ine ndinati: “Ndidzatchinjiriza njira zanga,+Kuti ndisachimwe ndi lilime langa.+Ndidzamanga pakamwa panga kuti patetezeke,+Nthawi zonse pamene woipa ali pamaso panga.”+ Yesaya 53:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iye anapanikizidwa+ ndipo analola kuti asautsidwe,+ koma sanatsegule pakamwa pake. Anatengedwa ngati nkhosa yopita kokaphedwa,+ ndipo mofanana ndi nkhosa yaikazi imene imakhala chete akamaimeta ubweya, nayenso sanatsegule pakamwa pake.+
39 Ine ndinati: “Ndidzatchinjiriza njira zanga,+Kuti ndisachimwe ndi lilime langa.+Ndidzamanga pakamwa panga kuti patetezeke,+Nthawi zonse pamene woipa ali pamaso panga.”+
7 Iye anapanikizidwa+ ndipo analola kuti asautsidwe,+ koma sanatsegule pakamwa pake. Anatengedwa ngati nkhosa yopita kokaphedwa,+ ndipo mofanana ndi nkhosa yaikazi imene imakhala chete akamaimeta ubweya, nayenso sanatsegule pakamwa pake.+