Mateyu 27:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iye anati: “Chifukwa chiyani? Kodi iyeyu walakwa chiyani?” Koma atatero m’pamene anawonjezera kufuula kuti: “Apachikidwe basi!”+ Maliko 15:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma Pilato anapitiriza kuwafunsa kuti: “Chifukwa chiyani? Kodi iyeyu walakwa chiyani?” Koma atatero m’pamene anawonjezera kufuula kuti: “M’pachikeni!”+
23 Iye anati: “Chifukwa chiyani? Kodi iyeyu walakwa chiyani?” Koma atatero m’pamene anawonjezera kufuula kuti: “Apachikidwe basi!”+
14 Koma Pilato anapitiriza kuwafunsa kuti: “Chifukwa chiyani? Kodi iyeyu walakwa chiyani?” Koma atatero m’pamene anawonjezera kufuula kuti: “M’pachikeni!”+