Maliko 15:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma Pilato anapitiriza kuwafunsa kuti: “Chifukwa chiyani? Kodi iyeyu walakwa chiyani?” Koma atatero m’pamene anawonjezera kufuula kuti: “M’pachikeni!”+ Luka 23:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Atamva izi, anayamba kumuumiriza mokweza mawu, ndi kumupempha kuti Yesu apachikidwe basi. Anthuwo anali kufuula mwamphamvu moti Pilato anangololera.+ Machitidwe 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mulungu wa Abulahamu, wa Isaki ndi wa Yakobo,+ Mulungu wa makolo athu, ndi amene walemekeza+ Mtumiki+ wake Yesu, amene inu munamupereka+ ndi kumukana pamaso pa Pilato, Pilatoyo akufuna kumumasula.+
14 Koma Pilato anapitiriza kuwafunsa kuti: “Chifukwa chiyani? Kodi iyeyu walakwa chiyani?” Koma atatero m’pamene anawonjezera kufuula kuti: “M’pachikeni!”+
23 Atamva izi, anayamba kumuumiriza mokweza mawu, ndi kumupempha kuti Yesu apachikidwe basi. Anthuwo anali kufuula mwamphamvu moti Pilato anangololera.+
13 Mulungu wa Abulahamu, wa Isaki ndi wa Yakobo,+ Mulungu wa makolo athu, ndi amene walemekeza+ Mtumiki+ wake Yesu, amene inu munamupereka+ ndi kumukana pamaso pa Pilato, Pilatoyo akufuna kumumasula.+