Ekisodo 23:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Usatsatire khamu pochita zoipa.+ Pa mlandu usapereke umboni wopotoza chilungamo potsatira khamu la anthu.+ Yohane 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma iwo anafuula kuti: “Muthane naye! Muthane naye! M’pachikeni!” Pilato anawafunsa kuti: “Kodi ndipachike mfumu yanu?” Ansembe aakulu anayankha kuti: “Tilibe mfumu ina koma Kaisara.”+
2 Usatsatire khamu pochita zoipa.+ Pa mlandu usapereke umboni wopotoza chilungamo potsatira khamu la anthu.+
15 Koma iwo anafuula kuti: “Muthane naye! Muthane naye! M’pachikeni!” Pilato anawafunsa kuti: “Kodi ndipachike mfumu yanu?” Ansembe aakulu anayankha kuti: “Tilibe mfumu ina koma Kaisara.”+