Genesis 49:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndodo yachifumu sidzachoka kwa Yuda,+ ndiponso chibonga cha wolamulira sichidzachoka pakati pa mapazi ake, kufikira Silo*+ atabwera. Ndipo mitundu ya anthu idzamumvera.+ Deuteronomo 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 uzidziikira mfumu imene Yehova Mulungu wako adzasankhe.+ Mfumu imene udzadziikire idzachokere pakati pa abale ako. Sudzaloledwa kudziikira mlendo amene si m’bale wako kukhala mfumu.
10 Ndodo yachifumu sidzachoka kwa Yuda,+ ndiponso chibonga cha wolamulira sichidzachoka pakati pa mapazi ake, kufikira Silo*+ atabwera. Ndipo mitundu ya anthu idzamumvera.+
15 uzidziikira mfumu imene Yehova Mulungu wako adzasankhe.+ Mfumu imene udzadziikire idzachokere pakati pa abale ako. Sudzaloledwa kudziikira mlendo amene si m’bale wako kukhala mfumu.