Maliko 15:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Yosefe wa ku Arimateya, munthu wodziwika wa m’Bungwe Lalikulu la Ayuda, amenenso anali kuyembekezera ufumu wa Mulungu,+ anapita kwa Pilato molimba mtima kukapempha mtembo+ wa Yesu. Luka 2:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndiyeno mu Yerusalemu munali munthu wina dzina lake Simiyoni. Mwamuna ameneyu anali wolungama ndi woopa Mulungu. Anali kuyembekezera nthawi imene Mulungu adzatonthoze Isiraeli,+ ndipo mzimu woyera unali pa iye.
43 Yosefe wa ku Arimateya, munthu wodziwika wa m’Bungwe Lalikulu la Ayuda, amenenso anali kuyembekezera ufumu wa Mulungu,+ anapita kwa Pilato molimba mtima kukapempha mtembo+ wa Yesu.
25 Ndiyeno mu Yerusalemu munali munthu wina dzina lake Simiyoni. Mwamuna ameneyu anali wolungama ndi woopa Mulungu. Anali kuyembekezera nthawi imene Mulungu adzatonthoze Isiraeli,+ ndipo mzimu woyera unali pa iye.