Mateyu 28:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndipo pitani mwamsanga mukauze ophunzira ake kuti wauka kwa akufa,+ moti padakali pano, watsogola kupita ku Galileya.+ Kumeneko mukamuona. Umenewutu ndi uthenga wanga kwa inu.”+ Maliko 16:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inuyo pitani, mukauze ophunzira ake komanso Petulo kuti, ‘Watsogola kupita ku Galileya.+ Kumeneko mukamuona, monga anakuuzirani.’”+
7 Ndipo pitani mwamsanga mukauze ophunzira ake kuti wauka kwa akufa,+ moti padakali pano, watsogola kupita ku Galileya.+ Kumeneko mukamuona. Umenewutu ndi uthenga wanga kwa inu.”+
7 Inuyo pitani, mukauze ophunzira ake komanso Petulo kuti, ‘Watsogola kupita ku Galileya.+ Kumeneko mukamuona, monga anakuuzirani.’”+