Mateyu 26:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Mu ola lomwelo Yesu anafunsa khamu la anthulo kuti: “Bwanji mwabwera kudzandigwira mutatenga malupanga ndi zibonga ngati mukukalimbana ndi wachifwamba?+ Tsiku ndi tsiku ndinali kukhala pansi m’kachisi+ ndi kuphunzitsa, koma simunandigwire.
55 Mu ola lomwelo Yesu anafunsa khamu la anthulo kuti: “Bwanji mwabwera kudzandigwira mutatenga malupanga ndi zibonga ngati mukukalimbana ndi wachifwamba?+ Tsiku ndi tsiku ndinali kukhala pansi m’kachisi+ ndi kuphunzitsa, koma simunandigwire.