Mateyu 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pa nthawiyo Herode,* wolamulira chigawo, anamva za Yesu+ Luka 23:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno, atadziwa kuti ndi wochokera m’chigawo cholamulidwa ndi Herode,*+ anamutumiza kwa Herode, amene m’masiku amenewo anali mu Yerusalemu.
7 Ndiyeno, atadziwa kuti ndi wochokera m’chigawo cholamulidwa ndi Herode,*+ anamutumiza kwa Herode, amene m’masiku amenewo anali mu Yerusalemu.