Mateyu 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 n’kumuuza kuti: “Ngati ndinu mwana wa Mulungu, mudziponye pansi,+ pajatu Malemba amati, ‘Iye adzalamula angelo ake za inu, ndipo adzakunyamulani m’manja mwawo, kuti phazi lanu lisawombe mwala uliwonse.’”+
6 n’kumuuza kuti: “Ngati ndinu mwana wa Mulungu, mudziponye pansi,+ pajatu Malemba amati, ‘Iye adzalamula angelo ake za inu, ndipo adzakunyamulani m’manja mwawo, kuti phazi lanu lisawombe mwala uliwonse.’”+