Mateyu 13:57 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 57 Choncho anayamba kukhumudwa naye.+ Koma Yesu anawauza kuti: “Mneneri salemekezedwa kwawo kapena m’nyumba mwake, koma kwina.”+ Maliko 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma Yesu anapitiriza kuwauza kuti: “Mneneri salemekezedwa kwawo,+ ngakhale ndi achibale ake, ngakhale m’nyumba mwake momwe, koma kwina.”+ Yohane 4:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Yesu mwiniyo anachitira umboni kuti mneneri salemekezedwa kwawo.+
57 Choncho anayamba kukhumudwa naye.+ Koma Yesu anawauza kuti: “Mneneri salemekezedwa kwawo kapena m’nyumba mwake, koma kwina.”+
4 Koma Yesu anapitiriza kuwauza kuti: “Mneneri salemekezedwa kwawo,+ ngakhale ndi achibale ake, ngakhale m’nyumba mwake momwe, koma kwina.”+