Mateyu 8:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano Yesu, atalowa m’nyumba mwa Petulo, anaona apongozi aakazi a Petulo+ ali gone, akudwala malungo.*+ Maliko 1:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Koma apongozi aakazi a Simoni+ anali chigonere, akudwala malungo.*+ Mwamsanga iwo anamuuza za mayiyo.
14 Tsopano Yesu, atalowa m’nyumba mwa Petulo, anaona apongozi aakazi a Petulo+ ali gone, akudwala malungo.*+
30 Koma apongozi aakazi a Simoni+ anali chigonere, akudwala malungo.*+ Mwamsanga iwo anamuuza za mayiyo.