Mateyu 4:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Atatero, anayendayenda+ m’Galileya+ yense kuphunzitsa m’masunagoge+ mwawo, kulalikira uthenga wabwino wa ufumu ndi kuchiritsa anthu matenda amtundu uliwonse+ ndi zofooka zilizonse. Maliko 1:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Iye anapitadi ndipo anali kulalikira m’masunagoge mwawo mu Galileya yense ndi kutulutsa ziwanda.+
23 Atatero, anayendayenda+ m’Galileya+ yense kuphunzitsa m’masunagoge+ mwawo, kulalikira uthenga wabwino wa ufumu ndi kuchiritsa anthu matenda amtundu uliwonse+ ndi zofooka zilizonse.