Mateyu 14:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Anthu anali kum’pempha kuti angogwira chabe ulusi wopota wa m’mphepete mwa malaya ake akunja,+ ndipo onse amene anaugwira anachiriratu.
36 Anthu anali kum’pempha kuti angogwira chabe ulusi wopota wa m’mphepete mwa malaya ake akunja,+ ndipo onse amene anaugwira anachiriratu.