Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 6:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 “‘Chilichonse chimene chingakhudze mnofu wake chidzakhala choyera,+ ndipo ngati munthu wadonthezera ena mwa magazi a nyamayo pachovala,+ chovala chimene wadonthezera magazicho muzichichapira kumalo oyera.+

  • Numeri 15:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 “Lankhula ndi ana a Isiraeli, uwauze kuti azisokerera mphonje m’mphepete mwa zovala zawo, ku mibadwo yawo yonse. Azisokereranso chingwe cha buluu pamwamba pa mphonje za zovalazo.+

  • Mateyu 9:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 chifukwa mumtima mwake anali kunena kuti: “Ndikangogwira malaya ake akunja okhawo, ndichira ndithu.”+

  • Maliko 3:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Popeza kuti anali atachiritsa anthu ambiri, onse amene anali ndi matenda aakulu anali kudziponya kwa iye kuti angomukhudza.+

  • Luka 6:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Onse m’khamulo anali kuyesetsa kuti amukhudze,+ chifukwa mphamvu+ zinali kutuluka mwa iye ndi kuchiritsa onsewo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena