Yesaya 40:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tamverani! Winawake akufuula m’chipululu kuti:+ “Konzani njira ya Yehova+ anthu inu! Wongolani msewu wa Mulungu wathu wodutsa m’chipululu.+ Mateyu 11:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Malemba amanena za iyeyu kuti, ‘Taona! Inetu ndikutumiza mthenga wanga choyamba, amene adzakukonzera njira!’+ Luka 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iye adzatembenuza ana ambiri a Isiraeli kuti abwerere kwa Yehova+ Mulungu wawo. Yohane 1:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iye anati: “Ndine mawu a winawake wofuula m’chipululu kuti, ‘Wongolani njira ya Yehova,’ monga mmene mneneri Yesaya ananenera.”+
3 Tamverani! Winawake akufuula m’chipululu kuti:+ “Konzani njira ya Yehova+ anthu inu! Wongolani msewu wa Mulungu wathu wodutsa m’chipululu.+
10 Malemba amanena za iyeyu kuti, ‘Taona! Inetu ndikutumiza mthenga wanga choyamba, amene adzakukonzera njira!’+
23 Iye anati: “Ndine mawu a winawake wofuula m’chipululu kuti, ‘Wongolani njira ya Yehova,’ monga mmene mneneri Yesaya ananenera.”+