Mateyu 11:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Kodi m’badwo uwu ndiufanizire ndi ndani?+ Uli ngati ana aang’ono amene amakhala pansi m’misika n’kumafuulira anzawo osewera nawo+
16 “Kodi m’badwo uwu ndiufanizire ndi ndani?+ Uli ngati ana aang’ono amene amakhala pansi m’misika n’kumafuulira anzawo osewera nawo+