Salimo 23:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mumandipatsa chakudya patebulo, pamaso pa anthu ondichitira zoipa.+Mwadzoza mutu wanga ndi mafuta.+Chikho changa ndi chodzaza bwino.+ Salimo 45:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Umakonda chilungamo+ ndipo umadana ndi zoipa.+N’chifukwa chake Mulungu, Mulungu wako,+ wakudzoza+ ndi mafuta achikondwerero chachikulu+ kuposa cha mafumu ena.+
5 Mumandipatsa chakudya patebulo, pamaso pa anthu ondichitira zoipa.+Mwadzoza mutu wanga ndi mafuta.+Chikho changa ndi chodzaza bwino.+
7 Umakonda chilungamo+ ndipo umadana ndi zoipa.+N’chifukwa chake Mulungu, Mulungu wako,+ wakudzoza+ ndi mafuta achikondwerero chachikulu+ kuposa cha mafumu ena.+