Mateyu 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 chifukwa mumtima mwake anali kunena kuti: “Ndikangogwira malaya ake akunja okhawo, ndichira ndithu.”+ Maliko 5:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Atamva zambiri zokhudza Yesu, anakalowa m’khamu la anthulo ndi kumudzera kumbuyo kwake, kenako anagwira+ malaya ake akunja.
21 chifukwa mumtima mwake anali kunena kuti: “Ndikangogwira malaya ake akunja okhawo, ndichira ndithu.”+
27 Atamva zambiri zokhudza Yesu, anakalowa m’khamu la anthulo ndi kumudzera kumbuyo kwake, kenako anagwira+ malaya ake akunja.