Maliko 5:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Nthawi yomweyonso, Yesu anamva m’thupi mwake kuti mphamvu+ yatulukamo. Pamenepo anatembenuka m’khamu la anthulo ndi kufunsa kuti: “Ndani wagwira malaya angawa?”+
30 Nthawi yomweyonso, Yesu anamva m’thupi mwake kuti mphamvu+ yatulukamo. Pamenepo anatembenuka m’khamu la anthulo ndi kufunsa kuti: “Ndani wagwira malaya angawa?”+