Mateyu 17:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Atasonkhana pamodzi ku Galileya, Yesu anawauza kuti: “Mwana wa munthu adzaperekedwa m’manja mwa anthu,+ Maliko 9:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Pakuti anali kuphunzitsa ophunzira ake ndi kuwauza kuti: “Mwana wa munthu adzaperekedwa m’manja mwa anthu, ndipo adzamupha,+ koma ngakhale adzamuphe, adzauka patapita masiku atatu.”+ Luka 18:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Mwachitsanzo, akamupereka kwa anthu a mitundu ina ndipo akamuseka,+ kum’chitira chipongwe+ ndi kumulavulira.+
22 Atasonkhana pamodzi ku Galileya, Yesu anawauza kuti: “Mwana wa munthu adzaperekedwa m’manja mwa anthu,+
31 Pakuti anali kuphunzitsa ophunzira ake ndi kuwauza kuti: “Mwana wa munthu adzaperekedwa m’manja mwa anthu, ndipo adzamupha,+ koma ngakhale adzamuphe, adzauka patapita masiku atatu.”+
32 Mwachitsanzo, akamupereka kwa anthu a mitundu ina ndipo akamuseka,+ kum’chitira chipongwe+ ndi kumulavulira.+