Salimo 22:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu onse ondiona amandinyodola.+Iwo amandinyogodola ndi pakamwa pawo, ndipo amapukusa mitu yawo mondinyoza.+ Iwo amati: Mateyu 27:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndipo atam’manga, anapita kukam’pereka kwa bwanamkubwa Pilato.+ Machitidwe 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mulungu wa Abulahamu, wa Isaki ndi wa Yakobo,+ Mulungu wa makolo athu, ndi amene walemekeza+ Mtumiki+ wake Yesu, amene inu munamupereka+ ndi kumukana pamaso pa Pilato, Pilatoyo akufuna kumumasula.+
7 Anthu onse ondiona amandinyodola.+Iwo amandinyogodola ndi pakamwa pawo, ndipo amapukusa mitu yawo mondinyoza.+ Iwo amati:
13 Mulungu wa Abulahamu, wa Isaki ndi wa Yakobo,+ Mulungu wa makolo athu, ndi amene walemekeza+ Mtumiki+ wake Yesu, amene inu munamupereka+ ndi kumukana pamaso pa Pilato, Pilatoyo akufuna kumumasula.+