Mateyu 20:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Akam’pereka kwa anthu a mitundu ina kuti am’chitire chipongwe, kum’kwapula ndi kum’pachika pamtengo,+ ndipo pa tsiku lachitatu adzaukitsidwa.”+ Luka 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pamenepo khamu lonselo linanyamuka, onse pamodzi, n’kupita naye kwa Pilato.+ Yohane 18:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno iwo anatenga Yesu kuchoka kwa Kayafako ndi kupita naye kunyumba ya bwanamkubwa.+ Umenewu unali m’mawa kwambiri. Koma iwo sanalowe m’nyumba ya bwanamkubwayo poopa kuipitsidwa.+ Iwo anali kufuna kuti akathe kudya pasika. Machitidwe 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mulungu wa Abulahamu, wa Isaki ndi wa Yakobo,+ Mulungu wa makolo athu, ndi amene walemekeza+ Mtumiki+ wake Yesu, amene inu munamupereka+ ndi kumukana pamaso pa Pilato, Pilatoyo akufuna kumumasula.+
19 Akam’pereka kwa anthu a mitundu ina kuti am’chitire chipongwe, kum’kwapula ndi kum’pachika pamtengo,+ ndipo pa tsiku lachitatu adzaukitsidwa.”+
28 Ndiyeno iwo anatenga Yesu kuchoka kwa Kayafako ndi kupita naye kunyumba ya bwanamkubwa.+ Umenewu unali m’mawa kwambiri. Koma iwo sanalowe m’nyumba ya bwanamkubwayo poopa kuipitsidwa.+ Iwo anali kufuna kuti akathe kudya pasika.
13 Mulungu wa Abulahamu, wa Isaki ndi wa Yakobo,+ Mulungu wa makolo athu, ndi amene walemekeza+ Mtumiki+ wake Yesu, amene inu munamupereka+ ndi kumukana pamaso pa Pilato, Pilatoyo akufuna kumumasula.+