Genesis 18:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kodi pali chosatheka ndi Yehova?+ Pa nthawi yoikidwiratu ndidzabweranso kwa iwe chaka chamawa. Ndidzabweranso nthawi ngati yomwe ino, ndipo Sara adzakhala ndi mwana wamwamuna.” Genesis 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Tsopano Yehova anakumbukira Sara monga mwa mawu ake, ndipo Yehovayo anachitira Sara monga momwe ananenera.+
14 Kodi pali chosatheka ndi Yehova?+ Pa nthawi yoikidwiratu ndidzabweranso kwa iwe chaka chamawa. Ndidzabweranso nthawi ngati yomwe ino, ndipo Sara adzakhala ndi mwana wamwamuna.”
21 Tsopano Yehova anakumbukira Sara monga mwa mawu ake, ndipo Yehovayo anachitira Sara monga momwe ananenera.+