Luka 6:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Pitirizani kukhala achifundo, potengera Atate wanu amenenso ali wachifundo.+ Yohane 13:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ngati zimenezi mukuzidziwa, ndinu odala mukamazichita.+ Aefeso 4:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Koma khalani okomerana mtima,+ achifundo chachikulu,+ okhululukirana ndi mtima wonse, monga mmene inunso Mulungu anakukhululukirani ndi mtima wonse kudzera mwa Khristu.+
32 Koma khalani okomerana mtima,+ achifundo chachikulu,+ okhululukirana ndi mtima wonse, monga mmene inunso Mulungu anakukhululukirani ndi mtima wonse kudzera mwa Khristu.+