1 Akorinto 7:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ndikunenatu zimenezi kuchitira ubwino wanu, osati kuti ndikuchititseni kukhala omangika, koma kuti ndikulimbikitseni kuchita choyenera+ ndiponso kutumikira Ambuye nthawi zonse popanda chododometsa.+
35 Ndikunenatu zimenezi kuchitira ubwino wanu, osati kuti ndikuchititseni kukhala omangika, koma kuti ndikulimbikitseni kuchita choyenera+ ndiponso kutumikira Ambuye nthawi zonse popanda chododometsa.+