Luka 18:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 ndionetsetsa kuti chilungamo chachitika kwa mkazi wamasiyeyu. Ndichita zimenezi kuti asapitirize kumangobwera ndi kundisautsa kwambiri,+ chifukwa mkazi ameneyu akundivutitsa+ mosalekeza.’”
5 ndionetsetsa kuti chilungamo chachitika kwa mkazi wamasiyeyu. Ndichita zimenezi kuti asapitirize kumangobwera ndi kundisautsa kwambiri,+ chifukwa mkazi ameneyu akundivutitsa+ mosalekeza.’”