Maliko 9:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Kenako Yohane anauza Yesu kuti: “Mphunzitsi, ife taona munthu wina akutulutsa ziwanda m’dzina lanu, choncho tinamuletsa,+ chifukwa sanali kuyenda ndi ife.”+ Luka 9:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Ndiyeno Yohane ananena kuti: “Mlangizi, tinaona munthu wina akutulutsa ziwanda+ m’dzina lanu, choncho ife tinamuletsa+ chifukwa sakukutsatirani pamodzi ndi ife.”+
38 Kenako Yohane anauza Yesu kuti: “Mphunzitsi, ife taona munthu wina akutulutsa ziwanda m’dzina lanu, choncho tinamuletsa,+ chifukwa sanali kuyenda ndi ife.”+
49 Ndiyeno Yohane ananena kuti: “Mlangizi, tinaona munthu wina akutulutsa ziwanda+ m’dzina lanu, choncho ife tinamuletsa+ chifukwa sakukutsatirani pamodzi ndi ife.”+