Numeri 11:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pamenepo, Yoswa mwana wa Nuni, yemwe anali mtumiki+ wa Mose kuyambira ali mnyamata, anayankhira kuti: “Mbuyanga Mose, kawaletseni amenewo!”+ Machitidwe 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma Ayuda ena oyendayenda amene anali kutulutsa ziwanda,+ anayesa kutchula dzina la Ambuye Yesu+ pofuna kuchiritsa anthu okhala ndi mizimu yoipa. Anali kunena kuti: “Ndikukulamulani+ mwa Yesu amene Paulo akumulalikira.”
28 Pamenepo, Yoswa mwana wa Nuni, yemwe anali mtumiki+ wa Mose kuyambira ali mnyamata, anayankhira kuti: “Mbuyanga Mose, kawaletseni amenewo!”+
13 Koma Ayuda ena oyendayenda amene anali kutulutsa ziwanda,+ anayesa kutchula dzina la Ambuye Yesu+ pofuna kuchiritsa anthu okhala ndi mizimu yoipa. Anali kunena kuti: “Ndikukulamulani+ mwa Yesu amene Paulo akumulalikira.”