Mateyu 28:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Maonekedwe ake anali ngati a mphezi,+ ndipo zovala zake zinali zoyera mbee!+